Translation of the song Malawian National Anthem - Mulungu dalitsa Malaŵi artist National Anthems & Patriotic Songs

Chewa

Malawian National Anthem - Mulungu dalitsa Malaŵi

English translation

Malawian National Anthem - O God bless our land of Malawi

Mlungu dalitsani Malaŵi,

O God bless our land of Malawi,

Mumsunge m'mtendere.

Keep it a land of peace.

Gonjetsani adani onse,

Put down each and every enemy,

Njala, nthenda, nsanje.

Hunger, disease, envy.

Lunzitsani mitima yathu,

Join together all our hearts as one,

Kuti tisaope.

That we be free from fear.

Mdalitse Mtsogoleri nafe,

Bless our leader, each and every one,

Ndi Mayi Malaŵi.

And Mother Malawi.

Malaŵi ndziko lokongola,

Our own Malawi, this land so fair,

La chonde ndi ufulu,

Fertile and brave and free.

Nyanja ndi mphepo ya m'mapiri,

With its lakes, refreshing mountain air,

Ndithudi tadala.

How greatly blest are we.

Zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu,

Hills and valleys, soil so rich and rare

N'mphatso zaulere.

Give us a bounty free.

Nkhalango, madambo abwino.

Wood and forest, plains so broad and fair,

Ngwokoma Malaŵi.

All - beauteous Malawi.

O Ufulu tigwirizane,

Freedom ever, let us all unite

Kukweza Malaŵi.

To build up Malawi.

Ndi chikondi, khama, kumvera,

With our love, our zeal and loyalty,

Timutumikire.

Bringing our best to her.

Pa nkhondo nkana pa mtendere,

In time of war, or in time of peace,

Cholinga n'chimodzi.

One purpose and one goal.

Mayi, bambo, tidzipereke,

Men and women serving selflessly

Pokweza Malaŵi.

In building Malawi.

0 130 0 Administrator

No comments!

Add comment